2 Samueli 11:13 BL92

13 Ndipo pakumuitana Davide, iyeyo anadya namwa pamaso pace; Davide namledzeretsa; ndipo usiku anaturuka kukagona pa kama wace pamodzi ndi anyamata a mbuye wace; koma sanatsildra ku nyumba yace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 11

Onani 2 Samueli 11:13 nkhani