25 Pomwepo Davide ananena ndi mthengawo, Udzatero kwa Yoabu, Cisakuipire ici, lupanga limaononga ina ndi mnzace. Onjeza kulimbitsa nkhondo yako pamudzipo, nuupasule; numlimbikitse motere.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 11
Onani 2 Samueli 11:25 nkhani