2 Samueli 11:27 BL92

27 Ndipo pakuturuka malirowo, Davide anatumiza munthu namtenga afike kwao ku nyumba yace; ndipo iyeyo anakhala mkazi wace nambalira mwana wamwamuna. Koma Yehova anaipidwa ndi cinthu cimene Davide adacita.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 11

Onani 2 Samueli 11:27 nkhani