2 Samueli 12:10 BL92

10 Cifukwa cace tsono lupanga silidzacoka pa nyumba yako nthawi zonse, popeza unandipeputsa Ine, nudzitengera mkazi wa Uriya Mhiti akhale mkazi wako.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 12

Onani 2 Samueli 12:10 nkhani