13 Ndipo Davide anati kwa Natani, Ndinacimwira Yehova. Natani nati kwa Davide, Ndiponso Yehova wacotsa chimo lanu, simudzafa.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 12
Onani 2 Samueli 12:13 nkhani