19 Koma pamene Davide anaona anyamata ace alikunong'onezana, Davide anazindikira kuti mwanayo adafa; Davide nanena ndi anyamata ace, Kodi mwanayo wafa? Nati iwo, Wafa.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 12
Onani 2 Samueli 12:19 nkhani