2 Samueli 12:4 BL92

4 Ndipo kwa wolemerayo kunafika mlendo, ndipo iye analeka kutengako mwa zoweta zace zazing'ono ndi zazikuru, kuphikira mlendo amene anafika kwa iye, koma anatenga mwana wa nkhosa wa wosaukayo, naphikira munthu amene anafika kwa iye.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 12

Onani 2 Samueli 12:4 nkhani