2 Samueli 14:13 BL92

13 Ndipo mkaziyo anati, Cifukwa ninjinso munalingalira cinthu cotere pa anthu a Mulungu? pakuti pakulankhula mau awa mfumu ikunga woparamula, popeza mfumu siitumiza okamtenganso woingidwa wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:13 nkhani