2 Samueli 14:18 BL92

18 Pamenepo mfumu inayankha, ninena naye mkaziyo, Usandibisire kanthu ka zimene ndidzakufunsa iwe. Mkaziyo nati, Mbuye wanga mfumu anene.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:18 nkhani