2 Samueli 14:2 BL92

2 Ndipo Yoabu anatumiza ku Tekowa, natenga kumeneko mkazi wanzeru, nanena naye, Ukokomezeke monga mfedwa, nubvale zobvala za pamaliro, osadzola mafuta, koma ukhale ngati munthu wamkazi wakulira akufa nthawi yaikuru.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:2 nkhani