2 Samueli 14:22 BL92

22 Ndipo Yoabu anagwa nkhope yace pansi, namlambira, nadalitsa mfumuyo; nati Yoabu, Lero mnyamata wanu ndadziwa kuti munandikomera mtima, mbuye wanga mfumu, popeza mfumu yacita copempha mnyamata wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:22 nkhani