2 Samueli 14:4 BL92

4 Ndipo pamene mkazi wa ku Tekowayo anati alankhule ndi mfumuyo, anagwa nkhope yace pansi namlambira, nati, Ndithandizeni mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:4 nkhani