2 Samueli 15:16 BL92

16 Mfumu nituruka, ndi banja lace lonse tinamtsata. Ndipo mfumu inasiya akazi khumi ndiwo akazi ang'ono, kusunga nyumbayo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:16 nkhani