2 Samueli 15:18 BL92

18 Ndipo anyamata ace onse anapita naye limodzi; ndi Akereri ndi Apeleti, ndi Agiti onse, anthu mazana asanu ndi limodzi omtsata kucokera ku Gati, anapita pamaso pa mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:18 nkhani