27 Ndipo mfumu inanenanso ndi Zadoki wansembeyo, Suli mlauli kodi? ubwere kumudzi mumtendere pamodzi ndi ana ako amuna awiri, Ahimaazi mwana wako ndi Jonatani mwana wa Abyatara.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15
Onani 2 Samueli 15:27 nkhani