2 Samueli 15:30 BL92

30 Ndipo Davide anakwera pa cikweza ca ku Azitona nakwera nalira misozi; ndipo anapfunda mutu wace nayenda ndi mapazi osabvala; ndi anthu onse amene anali naye anapfunda munthu yense mutu wace, ndipo anakwera, nalira misozi pokwerapo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:30 nkhani