2 Samueli 15:34 BL92

34 koma ukabwerera kumudzi, ndi kunena ndi Abisalomu, Ine ndine mnyamata wanu, mfumu; monga kale ndinali mnyamata wa atate wanu, momwemo tsopano ndidzakhala mnyamata wanu; pomwepo udzanditsutsira uphungu wa Ahitofeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:34 nkhani