2 Samueli 16:11 BL92

11 Ndipo Davide ananena ndi Abisai ndi anyamata ace onse, Onani, mwana wanga woturuka m'matumbo anga, alikufuna moyo wanga; koposa kotani nanga Mbenjamini uyu? mlekeni, atukwane, pakuti Yehova anamuuza.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 16

Onani 2 Samueli 16:11 nkhani