2 Samueli 16:13 BL92

13 Comweco Davide ndi anthu ace anapita m'ngra, ndipo Simeyi analambalala paphiri popenyana naye, namuka natukwana, namponya miyala, nawaza pfumbi,

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 16

Onani 2 Samueli 16:13 nkhani