2 Samueli 17:21 BL92

21 Ndipo kunali, atapita iwo, ajawo anaturuka m'citsime, namka nauza mfumu Davide; nati kwa Davide, Nyamukani nimuoloke madzi msanga; pakuti Ahitofeli anapangira zotere pa inu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17

Onani 2 Samueli 17:21 nkhani