2 Samueli 17:25 BL92

25 Ndipo Abisalomu anaika Amasa, kazembe wa khamulo, m'malo a Yoabu. Koma Amasayu ndiye mwana wa munthu dzina lace Itra M-israyeli, amene analowa kwa Abigayeli, mwana wamkazi wa Nahasi, mlongo wa Zeruya, amai a Yoabu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17

Onani 2 Samueli 17:25 nkhani