6 Ndipo pakufika Husai kwa Abisalomu, Abisalomuyo ananena naye, Ahitofeli analankhula mau akuti; ticite kodi monga mwa kunena kwace? ngati iai, unene ndiwe.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 17
Onani 2 Samueli 17:6 nkhani