2 Samueli 18:7 BL92

7 Ndipo anthu a Israyeli anakanthidwa pamenepo pamaso pa anyamata a Davide, ndipo kunali kuwapha kwakukuru kumeneko tsiku lomwelo, anthu zikwi makumi awiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 18

Onani 2 Samueli 18:7 nkhani