38 Ndipo mfumu inayankha, Cimamu adzaoloka nane, ndipo ndidzamcitira cimene cikukomereni; ndipo ciri conse mukadzapempha kwa ine ndidzakucitirani inu.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 19
Onani 2 Samueli 19:38 nkhani