2 Samueli 2:14 BL92

14 Ndipo Abineri ananena ndi Yoabu, Aimirire anyamata nasewere pamaso pathu. Nati Yoabu, Aimirire.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:14 nkhani