2 Samueli 2:16 BL92

16 Ndipo anagwirana munthu yense kugwira mutu wa mnzace, nagwaza ndi lupanga lace m'nthiti mwa mnzaceo Comweco anagwa limodzi; cifukwa cace malo aja anachedwa Dera la Mipeni la ku Gibeoni.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:16 nkhani