24 Koma Yoabu ndi Abisai anampitikitsa Abineri; ndipo dzuwa linawalowera pofika ku citunda ca Ama, cakuno ca Giya, pa njira ya ku cipululu ca Gibeoni.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2
Onani 2 Samueli 2:24 nkhani