2 Samueli 2:27 BL92

27 Yoabu nati, Pali Mulungu, iwe ukadapandakunena, anthu akadabalalika m'mawa osatsata yense mbale wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:27 nkhani