2 Samueli 2:30 BL92

30 Ndipo Yoabu anabwerera pakutsata Abineri. Ndipo pamene anasonkhanitsa pamodzi anthu onse anasowa anthu a Davide khumi ndi asanu ndi anai ndi Asaheli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 2

Onani 2 Samueli 2:30 nkhani