2 Samueli 20:12 BL92

12 Ndipo Amasa analikukunkhulira m'mwazi wace pakati pa mseu. Ndipo pamene munthuyo anaona kuti anthu onse anaima, iye ananyamula Amasa namcotsa pamseu kumka naye kuthengo, nampfunda ndi cobvala, pamene anaona kuti anaima munthu yense wakufika pali iye.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20

Onani 2 Samueli 20:12 nkhani