15 Ndipo anadza nammangira misasa m'Abeli wa Betimaaka, naundira nthumbira pa mudziwo, ndipo unagunda tioga; ndipo anthu onse akukhala ndi Yoabu anakumba lingalo kuti aligwetse.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20
Onani 2 Samueli 20:15 nkhani