19 Inendine wa awo amene ali amtendere ndi okhulupirika m'Israyeli; inu mulikufuna kuononga mudzi ndi mai wa m'Israyeli; mudzamezerang colowa ca Yehova?
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 20
Onani 2 Samueli 20:19 nkhani