2 Samueli 21:19 BL92

19 Ndipo panalinso nkhondo ndi Afilisti ku Gobu; ndipo Elhanani mwana wa Jare-oregimu wa ku Betelehemu anapha Goliate Mgiti, amene mtengo wa mkondo wace unanga mtanda wa woombera nsaru.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21

Onani 2 Samueli 21:19 nkhani