2 Samueli 21:4 BL92

4 Ndipo Agibeoni ananena naye, Sitifuna siliva kapena golidi wa Sauli kapena nyumba yace; ndiponso sitifuna kupha munthu ali yense wa m'Israyeli. Nati iye, Monga inu mudzanena, momwemo ndidzakucitirani.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21

Onani 2 Samueli 21:4 nkhani