7 Koma mfumu inaleka Mefiboseti mwana wa Jonatani, mwana wa Sauli, cifukwa ca lumbiro la kwa Yehova linali pakati pa Davide ndi Jonatani mwana wa Sauli.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 21
Onani 2 Samueli 21:7 nkhani