1 Ndipo Davide analankhula kwa Yehova mau a nyimbo iyi tsikuli Yehova anampulumutsa m'dzanja la adani ace onse, ndi m'dzanja la Sauli.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 22
Onani 2 Samueli 22:1 nkhani