2 Samueli 22:16 BL92

16 Pamenepo m'munsi mwa nyanja munaoneka,Maziko a dziko anaonekera poyera,Ndi mthonzo wa Yehova,Ndi mpumo wa mweya wa m'mphuno mwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 22

Onani 2 Samueli 22:16 nkhani