2 Samueli 23:1 BL92

1 Ndipo mau otsiriza a Davide ndi awa:—Atero Davide mwana wa Jese,Atero munthu wokwezedwa,Ndiye wodzozedwa wa Mulungu wa Yakobo,Ndi mwini masalmo wokoma wa Israyeli:

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 23

Onani 2 Samueli 23:1 nkhani