13 Ndipo atatu a mwamakumi atatu opambanawo, anatsika nafika kwa Davide nyengo ya kukolola m'phanga la ku Adulamu; ndi gulu la Afilisti Gnamanga zithando m'cigwa ca Refaimu.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 23
Onani 2 Samueli 23:13 nkhani