2 Samueli 24:17 BL92

17 Ndipo Davide analankhula ndi Yehova pamene anaona mthenga wakudwalitsa anthu, nati, Onani ndacimwa ine, ndinacita mwamphulupulu; koma nkhosa izi zinacitanji? dzanja lanu likhale pa ine ndi pa nyumba ya atate wanga.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 24

Onani 2 Samueli 24:17 nkhani