12 Ndipo Abineri anatuma mithenga imnenere kwa Davide, nati, Dziko nla yani? natinso, Mupangane nane pangano lanu, ndipo onani, ndidzagwirizana nanu ndi kukopa Aisrayeli onse atsate inu.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3
Onani 2 Samueli 3:12 nkhani