2 Samueli 3:14 BL92

14 Ndipo Davide anatumiza mithenga kwa Isiboseti mwana wa Sauli, nati, Undipatse mkazi wanga Mikala amene ndinadzitomera ndi nsonga za makungu za Afilisti zana limodzi.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3

Onani 2 Samueli 3:14 nkhani