16 Ndipo mwamuna waceyo anapita naye, nanka nalira, namtsata kufikira ku Baburimu. Pomwepo Abineri ananena naye, Coka, bwerera; ndipo anabwerera.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3
Onani 2 Samueli 3:16 nkhani