19 Ndipo Abineri analankhulanso m'kumva kwa Abenjamini; Abineri anamukanso ku Hebroni kulankhula m'makutu a Davide zonse zakukomera Aisrayeli ndi a nyumba yonse ya Benjamini.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3
Onani 2 Samueli 3:19 nkhani