2 Samueli 3:25 BL92

25 Mumdziwa Abineri mwana wa Neri kuti anadza kuti akunyengeni, ndi kuti adziwe kuturuka kwanu ndi kulowa kwanu, ndi kuti adziwe zonse mulikucita inu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3

Onani 2 Samueli 3:25 nkhani