2 Samueli 3:27 BL92

27 Pofikanso Abineri ku Hebroni, Yoabu anampambutsa kupita nave pakati pa cipata kulankhula naye poduka mphepo; namgwaza pomwepo m'mimba, nafa, cifukwa ca mwazi wa Asaheli mbale wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3

Onani 2 Samueli 3:27 nkhani