31 Ndipo Davide anati kwa Yoabu ndi kwa anthu onse okhala naye, Ng'ambani zobvala zanu, ndi kudzimangira ziguduli m'cuuno, nimulire Abineri. Ndipo mfumu Davide anatsata cithatha.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3
Onani 2 Samueli 3:31 nkhani