34 Manja anu sanamangidwa, mapazi anu sanalongedwa m'zigologolo;Monga munthu wakugwa ndi anthu oipa momwemo mudagwa inu.Ndipo anthu onse anamliranso.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3
Onani 2 Samueli 3:34 nkhani