39 Ndipo ndikali wofoka ine lero, cinkana ndinadzozedwa mfumu; ndipo amuna awa ana a Zeruya andikakalira mtima; Yehova abwezere wocita coipa monga mwa coipa cace.
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3
Onani 2 Samueli 3:39 nkhani