7 Ndipo Sauli adali ndi mkazi wamng'ono, dzina lace ndiye Rizipa, mwana wa Aya. Ndipo Isiboseti anati kwa Abineri, Unalowana bwanji ndi mkazi wamng'ono wa atate wanga?
Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 3
Onani 2 Samueli 3:7 nkhani